Kamba Ka Ine - Mystics

Kamba Ka Ine - Mystics
Kamba Ka Ine - Mystics
From the album The Conquest EP

Song Lyrics

Yes Lord, You are the King of Warriors

Jehovah Jireh

Jehovah Shalom

Ndinu ling langa

Yes, Lord, You are the God of peace

You mend the broken hearts

You heal every pain

Ndinu linga langa

Ndinu linga langa

You mend broken hearts

You heal every pain

Ndinu nokha Dada

Ndinu nokha Yahweh

HOOK

Munakwapulidwa, coz of my sins

Munanyozedwa, kamba ka ine

Munakwapulidwa, coz of my sins

Munanyozedwa

 

VERSE 2

Chipewa chaminga chikavwalikika kumutu kwinu Dada

Mphinjika mukanyamula kutimbika nthowa yose

Eeee Eeee

 

VERSE 3

Nkhondo, nkhondo Mbuye munandimenyera

Kwatsala nkwa ine kuti ndikutsateni.

Nkhondo, nkhondoMbuyemunatimenyera

Kwatsala nkwa ine kuti nditsate m’mapazi.