Intro
Ayiya
iyaye ehhh
Verse
1
M’mene
n’khalira moyo iwo samvetsa amadabwa nawo
(My lifestyle is a wonder to
many)
Pomwe
alira iyo ine Chimwemwe mumtsaya; sindilira mayo
(While they complain, I smile)
Ena
sapilira koma kufunsa chomwe ine nakumana nacho
(Some can’t hold it than to ask)
Kuti
moyo wangayu ukhale opatulika; osiyana nawo.
(What made my life different from
theirs)
Pre-chorus
Chimene
sodziwa n’choti ine ndimudziwa yemwe ndimudziwayo
(They don’t know that I know what
I know)
Komanso
sowona zoti ine ndimuwona yemwe ndimunanayo
(And they don’t know that I see
what I see)
Chorus
Ndili
nawo mwala womwe ndaponda ine
(I stand on the rock)
Yesu
ndi nthanthwe losasunthuka ayi
(Jesus in that unshakeable rock)
Ndili
nawo mwala womwe ndaponda ine
(I stand on the rock)
Yesu
ndi nthanthwe losasunthuka ayi
(Jesus in that unshakeable rock)
Verse
2
Anabwela
padziko kusiya ulemelero kudzapanga za ine
(He came on earth just for me)
Mwini
moyo wa moyo wosunga moyo wanga ndimapanga za iye
(I, too, mind Him; the giver and
sustained of life)
Chiyembekezo
adandipatsa, mantha adachotsa; ndiwopenso chiyani?
(He gave me hope, took away fear;
so why should I be afraid)
Adadzipeleka
yekha ngati msembe ya ochimwa, angandimane chiyani?
(He gave himself for a ransom;
What can He withhold from me)
Back
to chorus
Instruments
Back
to chorus