Mfumukazi - Chifuniro

Mfumukazi - Chifuniro
Mfumukazi - Chifuniro
From the album Maloto Anga

Song Lyrics

Verse 1.

Maso onse ali pa ife,

(All eyes on us)

Aliyense amve nkhani ya ife.

(Let all hear about us)

Kusakasaka kuja ndaleka,

(I am no longer searching for a lover)

Wabwera Mngelo wapa mtima panga.

(I am finally with my beloved angel)

Pa onse omwe ndawona

(From all the girls I have seen)

Iwe ndi Mfumukazi wa ine

(You are the queen of my heart)

Tsono mvetsera

(Now listen)

Tsogolo taliyamba.

(We have started off to our future)

 

Chorus

Ndilonjeza kudzakonda iwe,

(I promise to love you)

Ndidzakhala Mfumu ya iwe, ine.

(I will be you King)

Ndilonjeza kudzavera ine

(I promise to submit to you)

Ndidzakhala Mfumukazi ya iwe, ine.

(I will be you Queen)

Poti, Mulungu watikondera.

(For God has favoured us)

 

 

 

 

 

 

Verse 2.

Abusa atidalitse,

(May the priest bless us)

Ankhoswe asayinire za ife.

(Let the counsellors give consent)

Azinzathu asangalale

(Let friends rejoice)

Pachisankho chomwe tapanga ife

(On the choice we have made)

Pa chala chako, ndiyikapo Ring.

(On your finger, I place this ring)

Onse adziwe ndiwe wa ine,

(Letting everybody know; you are mine)

Tsono tawona,

(Now, take a look)

Tsogolo talifika.

(We are already in our future)

 

Back to Chorus.

 

Hook

Chomwe Mbuye wamanga, palibe wochimasula,

(What God joins, none put asunder)

Chikondi changa ndadzala palibe wodzachizula.

(I have planted my love in you, none will uproot it)

Ndidzakhala wa iwe,  popanda kukuDabula,

(I will forever be yours and see no one else)

Lonjezo langa kwa iwe, ndi ili ndilitchula;

(I hereby declare my promise to you)

 

Tsono tawona,

(Now, take a look)

Tsogolo talifika.

(We are already in our future)

 

Back to Chorus.