Lupanga (ft. Luko) - A'Chanza

Lupanga (ft. Luko) - A'Chanza
Lupanga (ft. Luko) - A'Chanza
From the album A'Chanza Singles

Song Lyrics

*LUPANGA*

*A'chanza ft. Luko*

Okay!
Your word sharper than double-edged sword yes you are
Munandidziwa ndithu nsanabadwe muta-
-lenga ine nati zili bwino mutha-
-ndizo lanu ndipedzadi mkhutho
oh God!
You breathed ur last pamtanda mau ndikudzatha
U gave ur life padziko patu ndikudzatha-
-ndizira moyo wanga nchitetezo ndinu TATA
For everything is vanity koma mau sadzatha
Kutivekadi mkanjo wa chiyero si inu sanza
Kutitchesa ndi mkate wa chiyero tchimo sanza
Poti inde pakutero tikhaladi anu son son
We serve the God of Galaxy tachiphula chi Samsung
The former glory is bigger but we waiting for the latter
We busy preaching and speaking of king lata-lata
Taking the whole kingdom by force tilalata
Kupanda kutinvera tilemberanso kalata

*CHORUS*
Mau anu sakhumudwitsa
Mau anu samagonja
Mau *2
Mau anu ndi Lupanga

V.2
Uh
We leaving no stone unturned tikumwaza
Okhazikika kaya intern imva mphwanga
Chipulumutso nchomwe ifeyo tikukamba
Tsegula khomo afuna iweee tchimo lapa
Yesu khristu akufuna aakulu ndi anafe
Ndinvere chonde Thini, Khili komanso Nafe
Pakuti tonse ndi amene iyeyo anafe-
-ra usakhale yosabereka nthaka iye anafetsa
Uthenga ngwa aliyense tipewe zomanazi
Ena akugawa Mango ena akugawa ma Nanazi🍍
Wiping up every sin bweretsa Tissue ya Nana's🧻
This Gospel for kids & for ur moms & for NanaZ
The former glory is bigger but we waiting for the latter
We busy preaching and speaking of Jesus lata-lata
We taking the whole kingdom by force tilalata
Kupanda kutinvera tilemberanso kalata

*CHORUS*


*Bridge*
Mau  anu amapatsa
Amakonda amachiza
Amateteza
Samagonja
Amachiza
Amapatsa

*CHORUS*