Sagona - Chifuniro

Sagona - Chifuniro
Sagona - Chifuniro
From the album Maloto Anga

Song Lyrics

Chorus

Iye sagona kapena kuwodzera

(He does not sleep nor slumber)

Iye nthawi zonse amapanga za ine

He is eternally concerned about me)

Kodi wina ndi uti angandikonde dere?

(Who else will love me like He does)?

Kodi wina ndi uti angandikonde dere?

(Who else will love me like He does)?

 

Verse

Wakhala ukulira kwa nthawi yayitali

(You have cried for so long)

Wamukhulupilira koma nyengo sizikusintha

(You have trusted in God, but the conditions remain unimproved)

Chiyembekezo mwa Iye chikuchepa

(Your hope in Him is dwindling)

Koma osataya mtima Mulungu wako asamala

(But hold on; Your God cares)

Wodziwa mawa lako

akupanga za iwe.

(He who knows your tomorrow is concerned about you)

 

Chorus 2

 

Iye sagona kapena kuwodzera

(He does not sleep nor slumber)

Iye nthawi zonse amapanga za ine

He is eternally concerned about you)

Kodi wina ndi uti angandikonde dere?

(Who else will love you like He does)?

Kodi wina ndi uti angandikonde dere?

(Who else will love you like He does)?

 

 

 

 

Hook

Wokhulupilika x8

(Faithful, He is)

Yesu wanga

(My Jesus)

Nthawi zonse.

(All the time)

 

Outro

Poti sagona

(For He does not sleep)

Kapena kuwodzera

(Nor slumber)

Iye nthawi zonse

(Every time)

Amapanga za ine

(He is concerned about me)

Kodi wina ndi uti

(Who else)

Angandikonde dere?

(Would love like that)?

Kodi wina ndi uti

(Who else)

Uuuuh